12 Ndiponso, Yesaya ati,Padzali muzu wa Jese,Ndi iye amene aukira kucita ufumu pa anthu amitundu;Iyeyo anthu amitundu adzamuyembekezera.
Werengani mutu wathunthu Aroma 15
Onani Aroma 15:12 nkhani