20 ndipo cotero ndinaciyesa cinthu caulemu kulalikira Uthenga Wabwino, pa malopo Kristu asanachulldwe kale, kuti ndisamange nyumba pa maziko a munthu wina.
Werengani mutu wathunthu Aroma 15
Onani Aroma 15:20 nkhani