Aroma 3:20 BL92

20 cifukwa kuti pamaso pace palibe munthu adzayesedwa wolungama ndi Debito za lamulo; pakuti ucimo udziwika ndi lamulo.

Werengani mutu wathunthu Aroma 3

Onani Aroma 3:20 nkhani