14 Komatu imfa inacita ufumu kuyambira kwa Adamu kufikira kwa Mose, ngakhale pa iwonso amene sanacimwa monga macimwidwe ace a Adamu, ndiye fanizo la wakudzayo.
Werengani mutu wathunthu Aroma 5
Onani Aroma 5:14 nkhani