19 Pakuti monga ndi kusamvera kwa munthu mmodzi ambiri anayesedwa ocimwa, comweco ndi kumvera kwa mmodzi ambiri adzayesedwa olungama.
Werengani mutu wathunthu Aroma 5
Onani Aroma 5:19 nkhani