1 Nanga kodi simudziwa, abale, pakuti ndilankhula ndi anthu akudziwa lamulo, kuti lamulolo licita ufumu pa munthu nthawi zonse iye ali wamoyo?
Werengani mutu wathunthu Aroma 7
Onani Aroma 7:1 nkhani