Aroma 7:15 BL92

15 Pakuti cimene ndicita sindicidziwa; pakuti sindicita cimene ndifuna, koma cimene ndidana naco, ndicita ici.

Werengani mutu wathunthu Aroma 7

Onani Aroma 7:15 nkhani