Aroma 7:23 BL92

23 koma ndiona lamulo lina m'ziwalo zanga, lirikulimbana ndi lamulo la mtima wanga, ndi kundigonjetsa kapolo wa lamulo la m'ziwalo zanga.

Werengani mutu wathunthu Aroma 7

Onani Aroma 7:23 nkhani