13 pakuti ngati mukhala ndi moyo monga mwa thupi, mudzafa; koma ngati ndi mzimu mufetsa zocita zace za thupi, mudzakhala ndi moyo.
Werengani mutu wathunthu Aroma 8
Onani Aroma 8:13 nkhani