28 Ndipo tidziwa kuti amene akonda Mulungu zinthu zonse zithandizana kuwacitira ubwino, ndiwo amene aitanidwa monga mwa kutsimikiza kwa mtima wace.
Werengani mutu wathunthu Aroma 8
Onani Aroma 8:28 nkhani