24 kuti, Tiri ndi ciani ife ndi Inu Yesu wa ku Nazarete? Kodi mwadza kudzationonga ife? Ndikudziwani, ndinu Woyerayo wa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Marko 1
Onani Marko 1:24 nkhani