19 Udziwa malamulo: Usaphe, Usacite cigololo, Usabe, Usacite umboni wakunama, Usanyenge, Lemekeza atate wako ndi amako.
Werengani mutu wathunthu Marko 10
Onani Marko 10:19 nkhani