Marko 10:38 BL92

38 Koma Yesu anati kwa iwo, Simudziwa cimene mucipempha, Mukhoza kodi kumwera cikho cimene ndimwera Ine? kapena kubatizidwa ndi ubatizo umene ndibatizidwa nao Ine?

Werengani mutu wathunthu Marko 10

Onani Marko 10:38 nkhani