Marko 10:42 BL92

42 Ndipo Yesu anawaitana, nanena nao, Mudziwa kuti iwo amene ayesedwa ambuye a mitundu ya anthu amacita ufumu pa iwo; ndipo akuru ao amacita ulamuliro pa iwo.

Werengani mutu wathunthu Marko 10

Onani Marko 10:42 nkhani