47 Ndipo pamene anamva kuti ndi Yesu wa ku Nazarete, anayamba kupfuula, ndi kunena, Yesu, Inu Mwana wa Davide, mundicitire ine cifundo.
Werengani mutu wathunthu Marko 10
Onani Marko 10:47 nkhani