49 Ndipo Yesu anaima, nati, Mwitaneni. Ndipo anaitana wakhunguyo, nanena naye, Limba mtima; nyamuka, akuitana.
Werengani mutu wathunthu Marko 10
Onani Marko 10:49 nkhani