52 Ndipo Yesu anati kwa iye, Muka; cikhulupiriro cako cakupulumutsa iwe. Ndipo pomwepo anapenyanso; namtsata Iye panjira.
Werengani mutu wathunthu Marko 10
Onani Marko 10:52 nkhani