Marko 11:17 BL92

17 Ndipo anaphunzitsa, nanena nao, Sicilembedwa kodi, Nyumba yanga idzachedwa nyumba yakupempheramo anthu a mitundu yonse? koma inu mwaiyesa phanga la acifwamba.

Werengani mutu wathunthu Marko 11

Onani Marko 11:17 nkhani