Marko 11:31 BL92

31 Ndipo anatsutsana mwa iwo okha, nanena, Tikati, Kumwamba; adzanena iye, Ndipo simunakhulupirira iye bwanji?

Werengani mutu wathunthu Marko 11

Onani Marko 11:31 nkhani