17 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Perekani zace za Kaisara kwa Kaisara, ndi zace za Mulungu kwa Mulungu. Ndipo anazizwa naye kwambiri.
Werengani mutu wathunthu Marko 12
Onani Marko 12:17 nkhani