Marko 13:1 BL92

1 Ndipo pamene analikuturuka Iye m'Kacisi, mmodzi wa ophunzira ace ananena kwa Iye, Mphunzitsi, onani, miyala yotere ndi nyumba yotere.

Werengani mutu wathunthu Marko 13

Onani Marko 13:1 nkhani