34 Monga ngati munthu wa paulendo, adacoka kunyumba kwace, nawapatsa akapolo ace ulamuliro, kwa munthu ali yense nchito yace, nalamulira wapakhomo adikire.
Werengani mutu wathunthu Marko 13
Onani Marko 13:34 nkhani