7 Ndipo m'mene mudzamva za nkhondo ndi mbiri zace za nkhondo, musamadera nkhawa: ziyenerakucitika izi; koma sicinafike cimariziro.
Werengani mutu wathunthu Marko 13
Onani Marko 13:7 nkhani