Marko 14:4 BL92

4 Koma anakhalako ena anabvutika mtima mwa iwo okha, ndi kuti, Mafutawo atayidwa cifukwa ninji?

Werengani mutu wathunthu Marko 14

Onani Marko 14:4 nkhani