Marko 14:40 BL92

40 Ndipo anadzanso nawapeza ali m'tulo, pakuti maso ao analemeradi; ndipo sanadziwa comyankha Iye.

Werengani mutu wathunthu Marko 14

Onani Marko 14:40 nkhani