14 Ndipo Pilato ananena nao, Pakuti Iye anacita coipa cotani? Koma iwo anapfuulitsatu, Mpacikeni Iye.
Werengani mutu wathunthu Marko 15
Onani Marko 15:14 nkhani