Marko 16:7 BL92

7 Koma mukani, uzani ophunzira ace, ndi Petro, kuti akutsogolerani inu ku Galileya; kumeneko mudzamuona Iye, monga ananena ndi inu.

Werengani mutu wathunthu Marko 16

Onani Marko 16:7 nkhani