Marko 2:16 BL92

16 Ndipo alembi a kwa Afarisi, pakuona kuti alinkudya nao ocimwa ndi amisonkho, ananena ndi ophunzira ace, Uyu akudya ndi kumwa nao amisonkho ndi ocimwa.

Werengani mutu wathunthu Marko 2

Onani Marko 2:16 nkhani