Marko 2:8 BL92

8 Ndipo pomwepo Yesu pozindikira mumtima mwace kuti alikuganizira comweco mwa iwo okha, ananena nao, Muganiza bwanji zinthu izi m'mitima yanu?

Werengani mutu wathunthu Marko 2

Onani Marko 2:8 nkhani