22 Ndipo alembi amene adatsika ku Yerusalemu ananena kuti, Ali naye Beelzibule, ndipo, Ndi mkuru wao wa ziwanda aturutsa ziwanda.
Werengani mutu wathunthu Marko 3
Onani Marko 3:22 nkhani