15 Ndipo iwo ndiwo a m'mbali mwa njira mofesedwamo mau; ndipo pamene anamva, pomwepo akudza Satana nacotsa mau ofesedwa mwa iwo.
Werengani mutu wathunthu Marko 4
Onani Marko 4:15 nkhani