24 Ndipo ananena nao, Yang'anirani cimene mukumva; ndi muyeso umene muyesera nao udzayesedwa kwa inu; ndipo kudzaonjezedwa kwa inu.
Werengani mutu wathunthu Marko 4
Onani Marko 4:24 nkhani