39 Ndipo anauka, nadzudzula mphepo, nati kwa nyanja, kuti, Tonthola, khala bata. Ndipo mphepo inaleka, ndipokunagwa bata lalikuru.
Werengani mutu wathunthu Marko 4
Onani Marko 4:39 nkhani