21 Ndipo pamene Yesu anaolokanso mungalawa tsidya lina, khamu lalikuru linasonkhana kwa Iye; ndipo Iye anali pambali pa nyanja.
Werengani mutu wathunthu Marko 5
Onani Marko 5:21 nkhani