Marko 5:33 BL92

33 Koma mkaziyo anacita mantha, ndi kunthunthumira, podziwa cimene anamcitira iye, nadza, namgwadira, namuuza coona conse.

Werengani mutu wathunthu Marko 5

Onani Marko 5:33 nkhani