1 Ndipo Iye anaturuka kumeneko; nafika ku dziko la kwao; ndipo ophunzira ace anamtsata.
Werengani mutu wathunthu Marko 6
Onani Marko 6:1 nkhani