Marko 6:15 BL92

15 Koma ena ananena, kuti, Ndiye Eliya, Anati enanso, Ndiye mneneri, monga ngati mmodzi wa aneneriwo,

Werengani mutu wathunthu Marko 6

Onani Marko 6:15 nkhani