25 Ndipo pomwepo analowa m'mangu m'mangu kwa mfumu, napempha kuti, Ndifuna kuti mundipatse tsopano apa, mutu wace wa Yohane Mbatizi mumbizi.
Werengani mutu wathunthu Marko 6
Onani Marko 6:25 nkhani