Marko 6:27 BL92

27 Ndipo pomwepo mfumu inatuma mnyamata, namlamulira akatenge mutu wace; ndipo iye anamuka namdula mutu m'nyumba yandende;

Werengani mutu wathunthu Marko 6

Onani Marko 6:27 nkhani