Marko 6:45 BL92

45 Ndipo pomwepo Iye anakangamiza ophunzira ace alowe rri'ngalawa, ndi kumtsogolera kutsidya lija ku Betsaida, m'mene Iye yekha alimkuuza khamulo kuti amuke.

Werengani mutu wathunthu Marko 6

Onani Marko 6:45 nkhani