Marko 7:18 BL92

18 Ndipo ananena nao, Mutero inunso opanda nzeru kodi? Kodi simuzindikira kuti kanthu kali konse kocokera kunja kakulowa mwa munthu, sikangathe kumdetsa iye;

Werengani mutu wathunthu Marko 7

Onani Marko 7:18 nkhani