26 Koma mkaziyo anali Mhelene, mtundu wace MsuroFonika. Ndipo anampempha Iye kuti aturutse ciwanda m'mwana wace.
Werengani mutu wathunthu Marko 7
Onani Marko 7:26 nkhani