Marko 9:18 BL92

18 ndipo ponse pamene umgwira, umgwetsa; ndipo acita thobvu, nakukuta mano, nanyololoka; ndipo ndinalankhula nao ophunzira anu kuti auturutse; koma sanakhoza.

Werengani mutu wathunthu Marko 9

Onani Marko 9:18 nkhani