28 Ndipo pamene Iye adalowa m'nyumba, ophunzira ace anamfunsa m'tseri, kuti, Nanga bwanji sitinakhoza ife kuuturutsa?
Werengani mutu wathunthu Marko 9
Onani Marko 9:28 nkhani