16 Koma asanafe, Davide adanena naye, Wadziphetsa ndi mtima wako; cifukwa pakamwa pako padacita umboni wakukutsutsa ndi kuti, Ine ndinapha wodzozedwa wa Yehova.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1
Onani 2 Samueli 1:16 nkhani