2 pa tsiku lacitatu, onani, munthu anaturuka ku zithando za Sauli, ali ndi zobvala zace zong'ambika, ndi dothi pamutu pace; ndipo kunatero kuti iye, pofika kwa Davide, anagwa pansi namgwadira.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 1
Onani 2 Samueli 1:2 nkhani