2 Samueli 10:14 BL92

14 Ndipo pamene ana a Amoni anaona kuti Aaramu anathawa, iwonso anathawa pamaso pa Abisai, nalowa m'mudzimo. Ndipo Yoabu anabwera kucokera kwa ana a Amoni, nafika ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:14 nkhani