2 Samueli 10:16 BL92

16 Ndipo Hadarezeri anatumiza mthenga nakatenga Aaramu a ku tsidya la cimtsinje; iwo nafika ku Helamu, ndi Sobaki kazembe wa khamu la nkhondo la Hadarezeri anawatsogolera.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:16 nkhani