2 Samueli 10:8 BL92

8 Ndipo ana a Amoni anaturuka, nandandalitsa nkhondo polowera kucipata. Ndipo Aaramu a ku Zoba ndi a ku Rehobu, ndi anthu a Tobu ndi Maaka, anali pa okha kuthengo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:8 nkhani