10 Ndipo pamene anauza Davide kuti, Uriya sanatsildra ku nyumba yace, Davide ananena ndi Uriya, Kodi sunabwera kuulendo? cifukwa ninji sunatsikira ku nyumba yako?
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11
Onani 2 Samueli 11:10 nkhani